Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 36:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma panali caka cakhumi ndi cinai ca mfumu Hezekiya, Sanakeribu, mfumu ya Asuri anadza, nathira nkhondo pa midzi ya malinga yonse ya Yuda, nailanda.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 36

Onani Yesaya 36:1 nkhani