Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 36:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu ya Asuri inatumiza kazembe kucokera pa Lakisi, kunka ku Yerusalemu, kwa mfumu Hezekiya, ndi nkhondo yambiri. Ndipo iye anaima cifupi ndi mcerenje wa thamanda la kumtunda, m'khwalala la pa mwaniko wa wotsuka nsaru.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 36

Onani Yesaya 36:2 nkhani