Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 31:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Iyenso ali wanzeru, nadzatengera coipa, ndipo sadzabwezanso mau ace, koma adzaukira banja la ocita zoipa, ndi amene athandiza iwo akugwira nchito yoipa.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 31

Onani Yesaya 31:2 nkhani