Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 30:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cikwi cimodzi cidzathawa pakuwadzudzula mmodzi; pakukudzudzulani anthu asanu mudzathawa; kufikira inu mudzasiyidwa ngati mlongoti pamwamba pa phiri, ndi ngati mbendera pamwamba pa citundu.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 30

Onani Yesaya 30:17 nkhani