Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 30:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma munati, Iai, pakuti tidzathawa pa akavalo; cifukwa cace inu mudzathawadi; ndipo ife tidzakwera pa akavalo aliwiro; cifukwa cace iwo amene akuthamangitsani, adzakhala aliwiro.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 30

Onani Yesaya 30:16 nkhani