Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 30:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace Yehova adzadikira, kuti akukomereni mtima, ndipo cifukwa cace Iye adzakuzidwa, kuti akucitireni inu cifundo; pakuti Yehova ndiye Mulungu wa ciweruziro; odala ali onse amene amdikira Iye.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 30

Onani Yesaya 30:18 nkhani