Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 25:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo adzanena tsiku limenelo, Taonani, uyu ndiye Mulungu wathu; tamlindirira Iye, adzatipulumutsa; uyu ndiye Yehova, tamlindirira Iye, tidzakondwa ndikusekereram'cipulumutso cace.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 25

Onani Yesaya 25:9 nkhani