Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 25:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iye wameza imfa ku nthawi yonse; ndipo Ambuye Mulungu adzapukuta misozi pa nkhope zonse; ndipo citonzo ca anthu ace adzacicotsa pa dziko lonse lapansi; cifukwa Yehova wanena.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 25

Onani Yesaya 25:8 nkhani