Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 25:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Iye adzaononga m'phiri limeneli cophimba nkhope cobvundikira mitundu yonse ya anthu, ndi nsaru yokuta amitundu onse.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 25

Onani Yesaya 25:7 nkhani