Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 25:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'phiri limendi Yehova wa makamu adzakonzera anthu ace onse phwando la zinthu zonona, phwando la vinyo wa pamitsokwe, la zinthu zonona za mafuta okha okha, la vinyo wansenga wokuntha bwino.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 25

Onani Yesaya 25:6 nkhani