Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 15:8-9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

8. Pakuti kulira kwamveka kuzungulira malire a Moabu; kukuwa kwace kwafikira ku Eglaimu, ndi kukuwa kwace kwafikira ku Beerelimu.

9. Pakuti madzi a Dimoni adzala mwazi; pakuti ndidzatengera zina pa! Dimoni, mkango pa iye amene anapulumuka ku Moabu, ndi pa otsala am'dziko.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 15