Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 14:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Ambuye adzamcitira cifundo Yakobo, ndipo adzasankhanso Israyeli, ndi kuwakhazikitsa m'dziko la kwao; ndipo acilendo adzadziphatika okha kwa iwo, nadzadzigumikiza ku nyumba ya Yakobo.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 14

Onani Yesaya 14:1 nkhani