Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 14:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mitundu ya anthu idzawatenga, ndi kuwafikitsa ku malo a kwao; ndipo a nyumba ya Israyeli adzakhala nao amitunduwo m'dziko la Yehova, ndi kuwayesa atumiki ndi adzakazi, ndipo amitunduwo adzatengedwa ndende, ndi amenewo anali ndende zao; ndipo Aisrayeli adzalamulira owabvuta.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 14

Onani Yesaya 14:2 nkhani