Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 11:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova adzaononga ndithu bondo la nyanja ya Aigupto; ndipo ndi mphepo yace yopsereza adzagwedeza dzanja lace pa Nyanja, ndipo adzaimenya ikhale mphaluka zisanu ndi ziwiri, nadzaolotsa anthu pansi pouma.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 11

Onani Yesaya 11:15 nkhani