Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 11:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo adzagudukira mapewa a Afilisti kumadzulo; pamodzi adzafunkha ana a kum'mawa; adzatambasula dzanja lao pa Edomu ndi pa Moabu; ndipo ana a Amoni adzawamvera.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 11

Onani Yesaya 11:14 nkhani