Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 51:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Israyeli ndi Yuda sasiyidwa ndi Mulungu wao, ndiye Yehova wa makamu: ngakhale dziko lao ladzala ndi ucimo kucimwira Woyera wa Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 51

Onani Yeremiya 51:5 nkhani