Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 51:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Thawani pakati pa Babulo, yense apulumuke moyo wace; musathedwe m'coipa cace; pakuti ndi nthawi ya kubwezera cilango; Yehova adzambwezera iye mphotho yace.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 51

Onani Yeremiya 51:6 nkhani