Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 50:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mau a iwo akuthawa akupulumuka m'dziko la Babulo, kuti alalikire m'Ziyoni kubwezera cilango kwa Yehova Mulungu wathu, kubwezera cilango cifukwa ca Kacisi wace.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 50

Onani Yeremiya 50:28 nkhani