Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 50:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Memezani amauta amenyane ndi Babulo, onse amene akoka uta; mummangire iye zitando pomzungulira iye, asapulumuke mmodzi wace yense; mumbwezere iye monga mwa nchito yace; monga mwa zonse wazicita, mumcitire iye; pakuti anamnyadira Yehova, Woyera wa Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 50

Onani Yeremiya 50:29 nkhani