Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 5:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Bwanji ndidzakhululukira iwe? pamenepo ana ako andisiya Ine, nalumbira pa iyo yosati milungu; pamene ndinakhutitsa iwo, anacita cigololo, nasonkhana masonkhano m'nyumba za adama.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 5

Onani Yeremiya 5:7 nkhani