Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 5:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace mkango woturuka m'nkhalango udzawapha, ndi mmbulu wa madzulo udzawafunkha, nyalugwe adzakhalira m'midzi mwao, onse amene aturukamo adzamwetulidwa; pakuti zolakwa ziri zambiri, ndi mabwerero ao acuruka.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 5

Onani Yeremiya 5:6 nkhani