Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 5:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ine ndidzanka kwa akuru, ndidzanena ndi iwo; pakuti adziwa njira ya Yehova, ndi ciweruzo ca Mulungu wao. Koma awa anabvomerezana natyola gori, nadula zomangira zao.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 5

Onani Yeremiya 5:5 nkhani