Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 49:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nyamukani, kwererani mtundu wokhala ndi mtendere, wokhala osadera nkhawa, ati Yehova, amene alibe zitseko ndi mipiringidzo, okhala pa okha.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 49

Onani Yeremiya 49:31 nkhani