Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 49:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kuwa, iwe Hesiboni, pakuti Ai wapasuka; lirani, inu ana akazi a Raba, mubvale ciguduli; citani maliro, thamangani kwina ndi kwina pamipanda; pakuti mfumu yao idzalowa m'ndende, ansembe ace ndi akuru ace pamodzi.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 49

Onani Yeremiya 49:3 nkhani