Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 46:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Usaope, iwe Yakobo mtumiki wanga, ati Yehova; pakuti Ine ndiri ndi iwe; pakuti Ine ndidzathetsa mitundu yonse kumene ndinakuingitsirako iwe, koma sindidzakuthetsa iwe; koma ndidzakulangiza ndi ciweruziro, ndipo sindidzakusiya konse wosalangidwa.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 46

Onani Yeremiya 46:28 nkhani