Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 46:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma usaope iwe, mtumiki wanga Yakobo, usacite mantha, iwe Israyeli: pakuti, taona, ndidzakupulumutsa iwe kucokera kutari, ndi mbeu yako ku dziko la undende wao, ndipo Yakobo adzabwera, nadzapumula m'mtendere, ndipo palibe amene adzamuopetsa iye,

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 46

Onani Yeremiya 46:27 nkhani