Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 46:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti tsikulo ndi la Ambuye, Yehova wa makamu, tsiku lakubweza cilango, kuti abwezere cilango adani ace; ndipo lupanga lidzadya, lidzakhuta, nilidzamwetsa mwazi wao; pakuti Ambuye, Yehova wa makamu, ali ndi nsembe m'dziko la kumpoto pa nyanja ya Firate.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 46

Onani Yeremiya 46:10 nkhani