Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 44:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo Yehova sanatha kupirirabe, cifukwa ca macitidwe anu oipa, ndi cifukwa ca zonyansa zimene munazicita; cifukwa cace dziko lanu likhala bwinja, ndi cizizwitso, ndi citemberero, lopanda wokhalamo, monga lero lomwe.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 44

Onani Yeremiya 44:22 nkhani