Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 44:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zofukizira zanu m'midzi ya Yuda, ndi m'miseu ya Yerusalemu, za inu ndi atate anu, mafumu anu ndi akuru anu, ndi anthu a m'dziko, kodi Yehova sanazikumbukira, kodi sizinalowa m'mtima mwace?

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 44

Onani Yeremiya 44:21 nkhani