Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 41:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Ismayeli mwana wa Netaniya anaturuka m'Mizipa kukakomana nao, alinkuyenda ndi kulira misozi; ndipo panali, pamene anakomana nao, anati kwa iwo, Idzani kwa Gedaliya mwana wace wa Ahikamu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 41

Onani Yeremiya 41:6 nkhani