Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 41:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

anadza anthu ocokera ku Sekemu, ndi ku Silo, ndi ku Samariya, anthu makumi asanu ndi atatu, atameta ndebvu zao, atang'amba zobvala zao, atadzitematema, ana tenga nsembe zaufa ndi zonunkhira m'manja mwao, kunka nazo ku nyumba ya Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 41

Onani Yeremiya 41:5 nkhani