Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 41:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali mwezi wacisanu ndi ciwiri, Ismayeli mwana wa Netaniya, mwana wa Elisama, wa mbeu ya mfumu, ndi kapitao wamkuru wa mfumu, ndi anthu khumi pamodzi ndi iye, anadza kwa Gedaliya mwana wa Ahikamu ku Mizipa; pamenepo anadya pamodzi m'Mizipa.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 41

Onani Yeremiya 41:1 nkhani