Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 41:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anauka Ismayeli mwana wa Netaniya, ndi anthu khumi okhala naye, namkantha Gedaliya mwana wa Ahikamu mwana wa Safani ndi lupanga, namupha iye, amene mfumu ya ku Babulo inamuika wolamulira dziko.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 41

Onani Yeremiya 41:2 nkhani