Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 4:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ndamva kubuula ngati kwa mkazi wobala, ndi msauko ngati wa mkazi wobala mwana wace woyamba, mau a mwana wamkazi wa Ziyoni wakupuma mosiyiza, wakutambasula manja ace, ndi kuti, Tsoka ine tsopano! pakuti moyo wanga walefuka cifukwa ca ambanda.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 4

Onani Yeremiya 4:31 nkhani