Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 38:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo adzaturutsira Akasidi akazi anu onse, ndi ana anu, ndipo simudzapulumuka m'manja ao, koma mudzagwidwa ndi dzanja la mfumu ya ku Babulo; ndipo mudzatenthetsa mudziwu ndi moto.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 38

Onani Yeremiya 38:23 nkhani