Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 36:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzamlanga iye ndi mbeu zace ndi atumiki ace cifukwa ca mphulupulu zao; ndipo ndidzawatengera iwo, ndi okhala m'Yerusalemu, ndi anthu a Yuda, zoipa zonse ndawanenera iwo, koma sanamvera.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 36

Onani Yeremiya 36:31 nkhani