Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 36:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace Yehova atero za Yehoyakimu mfumu ya Yuda: Adzasowa wokhala pa mpando wacifumu wa Davide; ndipo mtembo wace udzaponyedwa usana kunja kuli dzuwa, ndi usiku kuli cisanu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 36

Onani Yeremiya 36:30 nkhani