Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 36:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yeremiya anatenga mpukutu wina, naupereka kwa Baruki mlembi, mwana wa Neriya; amene analemba m'menemo ponena Yeremiya mau onse a m'buku lija Yehoyakimu mfumu ya Yuda analitentha m'moto; ndipo anaonjezapo mau ambiri oterewa.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 36

Onani Yeremiya 36:32 nkhani