Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 35:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mau a Yonadabu mwana wa Rekabu, amene anauza ana ace, asamwe vinyo, alikucitidwa, ndipo mpaka lero samamwa, pakuti amvera lamulo la kholo lao; koma Ine ndanena ndi inu, ndalawirira ndi kunena; koma simunandimvera Ine.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 35

Onani Yeremiya 35:14 nkhani