Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 35:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndatumanso kwa inu atumiki anga onse aneneri, ndalawirira ndi kuwatuma, kuti, Bwererani kuleka yense njira yace yoipa, konzani macitidwe anu, musatsate milungu yina kuitumikira, ndipo mudzakhala m'dziko limene ndakupatsani inu ndi makolo anu; koma simunandichera khutu lanu, simunandimvera Ine.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 35

Onani Yeremiya 35:15 nkhani