Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 35:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli: Pita, nunene kwa anthu a Yuda ndi kwa okhala m'Yerusalemu, Kodi simudzalola kulangizidwa kumvera mau anga ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 35

Onani Yeremiya 35:13 nkhani