Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 34:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo iwe sudzapulumuka m'dzanja lace, koma udzagwiridwadi, nudzaperekedwa m'dzanja lace; ndipo maso ako adzaanana nao a mfumu ya ku Babulo, ndipo iye adzanena nawe pakamwa ndi pakamwa, ndipo udzanka ku Babulo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 34

Onani Yeremiya 34:3 nkhani