Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 34:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova Mulungu wa Israyeli atero, Pita, nena kwa Zedekiya mfumu ya Yuda, numuuze iye, kuti Yehova atero, Taona, ndidzapereka mudziwu m'dzanja la mfumu ya ku Babulo, ndipo adzautentha ndi moto;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 34

Onani Yeremiya 34:2 nkhani