Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 34:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mau amene anadza kwa Yeremiya kucokera kwa Yehova, pamene Nebukadinezara mfumu ya Babulo, ndi nkhondo yace yonse, ndi maufumu onse a dziko lapansi amene anagwira mwendo wace, ndi anthu onse, anamenyana ndi Yerusalemu, ndi midzi yace yonse, akuti:

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 34

Onani Yeremiya 34:1 nkhani