Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 33:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

M'midzi ya kumtunda, m'midzi ya kucidikha, m'midzi ya ku Mwera, m'dziko la Benjamini, m'malo ozungulira Yerusalemu, m'midzi ya Yuda, zoweta zidzapitanso pansi pa manja a iye amene aziwerenga, ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 33

Onani Yeremiya 33:13 nkhani