Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 33:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzayesa mudzi uno cifukwa ca kukondwa, ndi ciyamiko ndi ulemerero, pamaso pa amitundu onse a pa dziko lapansi, amene adzamva zabwino zonse ndidzawacitirazo, ndipo adzaopa nadzanthunthumira cifukwa ca zabwino zonse ndi mtendere wonse zimene ndidzaucitira.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 33

Onani Yeremiya 33:9 nkhani