Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 31:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo sadzaphunzitsa yense mnansi wace, ndi yense mbale wace, kuti, Mudziwe Yehova; pakuti iwo onse adzandidziwa, kuyambira wamng'ono kufikira wamkuru wa iwo, ati Yehova; pakuti ndidzakhululukira mphulupulu yao, ndipo sindidzakumbukira cimo lao.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 31

Onani Yeremiya 31:34 nkhani