Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 31:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ili ndi pangano limene ndidzapangana ndi nyumba ya Israyeli atapita masiku aja, ati Yehova; ndidzaika cilamulo canga m'kati mwao, ndipo m'mtima mwao ndidzacilemba; ndipo ndidzakhala Mulungu wao, nadzakhala iwo anthu anga;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 31

Onani Yeremiya 31:33 nkhani