Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 31:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova atero, amene apatsa dzuwa kuti liunikire usana, ndi malemba a mwezi ndi a nyenyezi kuti aunikire usiku, amene atonthoza nyanja, pamene mafunde ace agabvira; Yehova wa makamu ndi dzina lace:

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 31

Onani Yeremiya 31:35 nkhani