Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 31:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taimitsa zizindikiro, udzipangire zosonyeza; taika mtima wako kuyang'anira mseu wounda, njira imene unapitamo; tatembenukanso, iwe namwali wa Israyeli, tatembenukiranso ku midzi yako iyi.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 31

Onani Yeremiya 31:21 nkhani